Salimo 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzatamanda Yehova chifukwa cha chilungamo chake.+Ndidzaimba nyimbo motsatizana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda dzina+ la Yehova Wam’mwambamwamba.+ Salimo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzakutamandani inu Yehova ndi mtima wanga wonse.+Ndidzalengeza ntchito zanu zonse zodabwitsa.+ Salimo 51:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Inu Yehova, tsegulani milomo yangayi,+Kuti pakamwa panga patamande inu.+ Aheberi 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+
17 Ndidzatamanda Yehova chifukwa cha chilungamo chake.+Ndidzaimba nyimbo motsatizana ndi zipangizo zoimbira, kutamanda dzina+ la Yehova Wam’mwambamwamba.+
15 Kudzera mwa iye, tiyeni nthawi zonse tizitamanda Mulungu. Tizichita zimenezi monga nsembe imene tikupereka kwa Mulungu,+ yomwe ndi chipatso cha milomo yathu.+ Timagwiritsa ntchito milomo imeneyi polengeza dzina lake kwa anthu ena.+