Salimo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma inu Yehova ndinu chishango changa,+Ulemerero wanga+ ndiponso Wonditukula mutu.+ Salimo 37:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Yehova adzawathandiza ndi kuwapulumutsa.+Adzawapulumutsa kwa anthu oipa ndi kuwalanditsa,+Chifukwa athawira kwa iye.+ Salimo 40:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Yehova amandiwerengera.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Mulungu wanga musachedwe.+ Salimo 70:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Inu Mulungu, chitanipo kanthu mwamsanga kuti zinthu zindiyendere bwino.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Yehova musachedwe.+ Salimo 144:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye amandisonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndipo ndiye malo anga achitetezo,+Malo anga okwezeka ndi Wopereka chipulumutso,+Chishango+ changa ndi malo anga othawirako.+Iye amandigonjetsera mitundu ya anthu.+
40 Yehova adzawathandiza ndi kuwapulumutsa.+Adzawapulumutsa kwa anthu oipa ndi kuwalanditsa,+Chifukwa athawira kwa iye.+
17 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Yehova amandiwerengera.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Mulungu wanga musachedwe.+
5 Koma ine ndasautsika ndipo ndasauka.+Inu Mulungu, chitanipo kanthu mwamsanga kuti zinthu zindiyendere bwino.+Inu ndinu thandizo langa ndi Wopereka chipulumutso kwa ine.+Inu Yehova musachedwe.+
2 Iye amandisonyeza kukoma mtima kwake kosatha ndipo ndiye malo anga achitetezo,+Malo anga okwezeka ndi Wopereka chipulumutso,+Chishango+ changa ndi malo anga othawirako.+Iye amandigonjetsera mitundu ya anthu.+