Ekisodo 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+ Ekisodo 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.” Ekisodo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo mundipangire malo opatulika, popeza ndiyenera kukhala pakati panu.+ Ekisodo 29:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Choncho ndidzakhala pakati pa ana a Isiraeli, ndipo ndidzakhala Mulungu wawo.+ Deuteronomo 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Mose ndi ansembe achilevi analankhula ndi Aisiraeli onse kuti: “Aisiraeli inu, khalani chete ndi kumvetsera. Lero mwakhala anthu a Yehova Mulungu wanu.+ Deuteronomo 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti gawo la Yehova ndilo anthu ake.+Yakobo ndiye gawo la cholowa chake.+
7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+
6 Inuyo mudzakhala ufumu wanga wa ansembe ndi mtundu wanga woyera.’+ Ukanene mawu amenewa kwa ana a Isiraeli.”
9 Kenako Mose ndi ansembe achilevi analankhula ndi Aisiraeli onse kuti: “Aisiraeli inu, khalani chete ndi kumvetsera. Lero mwakhala anthu a Yehova Mulungu wanu.+