Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Yehova ndiye gawo langa, gawo limene ndinapatsidwa,+ komanso chikho changa.+

      Inu mukundisungira bwino kwambiri cholowa changa.

  • Salimo 73:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Thupi langa ndi mtima wanga zalefuka.+

      Mulungu ndiye thanthwe la mtima wanga ndiponso cholowa changa mpaka kalekale.+

  • Yeremiya 10:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma Mulungu wa Yakobo+ sali ngati mafanowa. Iye ndi amene anapanga china chilichonse.+ Isiraeli ndiye ndodo ya cholowa chake.+ Dzina la Mulunguyo ndi Yehova wa makamu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena