Salimo 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzakutamandani inu Yehova ndi mtima wanga wonse.+Ndidzalengeza ntchito zanu zonse zodabwitsa.+ Salimo 86:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndikukutamandani inu Yehova Mulungu wanga ndi mtima wanga wonse,+Ndipo ndidzalemekeza dzina lanu mpaka kalekale,
12 Ndikukutamandani inu Yehova Mulungu wanga ndi mtima wanga wonse,+Ndipo ndidzalemekeza dzina lanu mpaka kalekale,