1 Mafumu 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo+ analephera kupitiriza kutumikira,+ popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+ Salimo 57:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Inu Mulungu, kwezekani kupitirira kumwamba.+Ulemerero wanu ukhale pamwamba pa dziko lonse lapansi.+ Salimo 104:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ulemerero wa Yehova udzakhalapobe mpaka kalekale.+Yehova adzakondwera ndi ntchito zake.+
11 Chifukwa cha mtambowo, ansembewo+ analephera kupitiriza kutumikira,+ popeza ulemerero+ wa Yehova unadzaza nyumba ya Yehovayo.+
5 Inu Mulungu, kwezekani kupitirira kumwamba.+Ulemerero wanu ukhale pamwamba pa dziko lonse lapansi.+