Salimo 36:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ali pabedi lake amakonza chiwembu kuti apweteke anzake.+Amaima panjira yoipa.+Sapewa kuchita zinthu zoipa.+ Salimo 64:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Amafunafuna kuchita zinthu zosalungama,+Abisa chiwembu chimene achikonza mochenjera,+Ndipo zamkati, zamumtima mwa aliyense, n’zovuta kuzimvetsa.+ Miyambo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 mtima wokonzera ena ziwembu,+ mapazi othamangira kukachita zoipa,+ Zekariya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye,+ mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosautsika.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+ Mateyu 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+
4 Ali pabedi lake amakonza chiwembu kuti apweteke anzake.+Amaima panjira yoipa.+Sapewa kuchita zinthu zoipa.+
6 Amafunafuna kuchita zinthu zosalungama,+Abisa chiwembu chimene achikonza mochenjera,+Ndipo zamkati, zamumtima mwa aliyense, n’zovuta kuzimvetsa.+
10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye,+ mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosautsika.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+
28 Koma ine ndikukuuzani kuti aliyense woyang’anitsitsa mkazi+ mpaka kumulakalaka, wachita naye kale chigololo+ mumtima mwake.+