Salimo 17:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndisungeni monga mwana wa diso,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu,+ Salimo 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musalole kuti phazi la anthu odzikweza lindipondereze.+Ndipo musalole dzanja la anthu oipa kundipitikitsa kuti ndikhale wothawathawa.+ Salimo 37:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Yehova sadzasiya wolungama m’manja mwa woipayo,+Ndipo pamene wolungamayo akuweruzidwa, Mulungu sadzamuona monga wolakwa.+
8 Ndisungeni monga mwana wa diso,+Ndibiseni mumthunzi wa mapiko anu,+ Salimo 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Musalole kuti phazi la anthu odzikweza lindipondereze.+Ndipo musalole dzanja la anthu oipa kundipitikitsa kuti ndikhale wothawathawa.+ Salimo 37:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma Yehova sadzasiya wolungama m’manja mwa woipayo,+Ndipo pamene wolungamayo akuweruzidwa, Mulungu sadzamuona monga wolakwa.+
11 Musalole kuti phazi la anthu odzikweza lindipondereze.+Ndipo musalole dzanja la anthu oipa kundipitikitsa kuti ndikhale wothawathawa.+
33 Koma Yehova sadzasiya wolungama m’manja mwa woipayo,+Ndipo pamene wolungamayo akuweruzidwa, Mulungu sadzamuona monga wolakwa.+