Yobu 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pakuti iye amadziwa bwino njira imene ine ndimadutsa.+Akamaliza kundiyesa, ndidzakhala ngati golide.+ Salimo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amadziwa njira za olungama,+Koma oipa adzatheratu pamodzi ndi njira zawo.+ Salimo 119:105 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 105 Mawu anu ndi nyale younikira kumapazi anga,+Ndi kuwala kounikira njira yanga.+
10 Pakuti iye amadziwa bwino njira imene ine ndimadutsa.+Akamaliza kundiyesa, ndidzakhala ngati golide.+