Salimo 37:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Yehova adzawathandiza ndi kuwapulumutsa.+Adzawapulumutsa kwa anthu oipa ndi kuwalanditsa,+Chifukwa athawira kwa iye.+ Salimo 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pa tsiku la nsautso undiitane.+Ine ndidzakulanditsa, ndipo iwe udzandilemekeza.”+ Salimo 91:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+
40 Yehova adzawathandiza ndi kuwapulumutsa.+Adzawapulumutsa kwa anthu oipa ndi kuwalanditsa,+Chifukwa athawira kwa iye.+
15 Adzandiitana ndipo ndidzamuyankha.+Ndidzakhala naye m’nthawi ya masautso.+Ndidzamupulumutsa ndi kumupatsa ulemerero.+