Miyambo 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wokana kusunga mawu,+ wangongole adzamulanda chikole. Koma munthu amene amaopa lamulo ndiye adzalandire mphoto.+ Miyambo 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Aliyense wokana malangizo+ amakana moyo wake, koma munthu womvetsera chidzudzulo amakhala ndi mtima wanzeru.+
13 Wokana kusunga mawu,+ wangongole adzamulanda chikole. Koma munthu amene amaopa lamulo ndiye adzalandire mphoto.+
32 Aliyense wokana malangizo+ amakana moyo wake, koma munthu womvetsera chidzudzulo amakhala ndi mtima wanzeru.+