Miyambo 3:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Nthawi iliyonse ukagona sudzaopa chilichonse.+ Udzagona ndithu, ndipo tulo tako tidzakhala tokoma.+ Mlaliki 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wotumikira munthu wina amagona tulo tokoma+ ngakhale adye zochepa kapena zambiri. Koma zambiri zimene munthu wolemera amakhala nazo zimamulepheretsa kugona. Mateyu 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Odala ndi anthu amene akumva njala ndi ludzu+ la chilungamo, chifukwa adzakhuta.+
24 Nthawi iliyonse ukagona sudzaopa chilichonse.+ Udzagona ndithu, ndipo tulo tako tidzakhala tokoma.+
12 Wotumikira munthu wina amagona tulo tokoma+ ngakhale adye zochepa kapena zambiri. Koma zambiri zimene munthu wolemera amakhala nazo zimamulepheretsa kugona.