Genesis 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa chifukwa chimenechi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake,+ n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo iwo adzakhala thupi limodzi.+ Miyambo 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kasupe wa madzi ako akhale wodalitsidwa,+ ndipo usangalale ndi mkazi wapaunyamata wako.+ Yeremiya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano wayamba kundiitana kuti, ‘Atate wanga,+ ndinu bwenzi langa lapamtima kuyambira pa unyamata wanga.+
24 Pa chifukwa chimenechi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake,+ n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo iwo adzakhala thupi limodzi.+
4 Tsopano wayamba kundiitana kuti, ‘Atate wanga,+ ndinu bwenzi langa lapamtima kuyambira pa unyamata wanga.+