Salimo 45:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiwedi wokongola kwambiri kuposa ana a anthu.+Mawu otuluka m’kamwa mwako ndi osangalatsadi.+N’chifukwa chake Mulungu adzakupatsa madalitso mpaka kalekale.+ Miyambo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Milomo yolungama imasangalatsa mfumu yaikulu,+ ndipo mfumuyo imakonda munthu wolankhula zinthu zowongoka.+
2 Ndiwedi wokongola kwambiri kuposa ana a anthu.+Mawu otuluka m’kamwa mwako ndi osangalatsadi.+N’chifukwa chake Mulungu adzakupatsa madalitso mpaka kalekale.+
13 Milomo yolungama imasangalatsa mfumu yaikulu,+ ndipo mfumuyo imakonda munthu wolankhula zinthu zowongoka.+