1 Samueli 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Davide anadziwa kuti Sauli akumukonzera chiwembu.+ Choncho anauza Abiyatara wansembe kuti: “Bweretsa efodi kuno.”+ Salimo 38:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu amene akufuna kundiwononga anditchera misampha,+Amene akufuna kundivulaza akulankhula motsutsana nane,+Ndipo amakhala akukonza zachinyengo tsiku lonse.+ Miyambo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akamanena kuti: “Tiye tipitire limodzi. Tiye tikabisalire anthu kuti tikakhetse magazi.+ Tiye tikabisalire anthu osalakwa. Tikachite zimenezo popanda chifukwa chilichonse.+ Miyambo 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Mtima wa munthu wolungama umayamba waganiza usanayankhe,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamasefukira zoipa.+ Mateyu 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anali kupangana+ zoti agwire Yesu mochenjera ndi kumupha.
9 Davide anadziwa kuti Sauli akumukonzera chiwembu.+ Choncho anauza Abiyatara wansembe kuti: “Bweretsa efodi kuno.”+
12 Anthu amene akufuna kundiwononga anditchera misampha,+Amene akufuna kundivulaza akulankhula motsutsana nane,+Ndipo amakhala akukonza zachinyengo tsiku lonse.+
11 Akamanena kuti: “Tiye tipitire limodzi. Tiye tikabisalire anthu kuti tikakhetse magazi.+ Tiye tikabisalire anthu osalakwa. Tikachite zimenezo popanda chifukwa chilichonse.+
28 Mtima wa munthu wolungama umayamba waganiza usanayankhe,+ koma pakamwa pa anthu oipa pamasefukira zoipa.+