1 Mafumu 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ankalankhula miyambi 3,000+ ndipo nyimbo zake+ zinakwana 1,005. Miyambo 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Miyambi+ ya Solomo+ mwana wa Davide,+ mfumu ya Isiraeli,+ Miyambo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+ Mlaliki 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuwonjezera pa kukhala ndi nzeru,+ wosonkhanitsayo nthawi zonse anali kuphunzitsanso anthuwo kuti adziwe zinthu.+ Anali kusinkhasinkha ndi kufufuza zinthu mosamala,+ ndipo analemba miyambi yambiri m’ndondomeko yoyenera.+
10 Miyambi ya Solomo.+ Mwana wanzeru amakondweretsa bambo ake,+ koma mwana wopusa amamvetsa chisoni mayi ake.+
9 Kuwonjezera pa kukhala ndi nzeru,+ wosonkhanitsayo nthawi zonse anali kuphunzitsanso anthuwo kuti adziwe zinthu.+ Anali kusinkhasinkha ndi kufufuza zinthu mosamala,+ ndipo analemba miyambi yambiri m’ndondomeko yoyenera.+