Miyambo 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 komanso ukaitana kumvetsa zinthu+ ndi kufuulira kuzindikira,+ Miyambo 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kwa wopusa, kusonyeza khalidwe lotayirira kuli ngati masewera,+ koma nzeru zimakhala ndi munthu wozindikira.+
23 Kwa wopusa, kusonyeza khalidwe lotayirira kuli ngati masewera,+ koma nzeru zimakhala ndi munthu wozindikira.+