1 Mbiri 15:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma Davide+ ndi akulu a Isiraeli+ ndiponso atsogoleri+a anthu 1,000 aliyense, anali kuyenda mosangalala+ kupita kunyumba kwa Obedi-edomu,+ kukatenga likasa la pangano la Yehova. Miyambo 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mudzi umakondwera chifukwa cha makhalidwe abwino a anthu olungama,+ koma anthu oipa akawonongeka pamakhala mfuu yachisangalalo.+
25 Koma Davide+ ndi akulu a Isiraeli+ ndiponso atsogoleri+a anthu 1,000 aliyense, anali kuyenda mosangalala+ kupita kunyumba kwa Obedi-edomu,+ kukatenga likasa la pangano la Yehova.
10 Mudzi umakondwera chifukwa cha makhalidwe abwino a anthu olungama,+ koma anthu oipa akawonongeka pamakhala mfuu yachisangalalo.+