Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 15:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndipo pamene amuna anali kuimba, Miriamu anathirira mang’ombe kuti:+

      “Imbirani Yehova+ pakuti wakwezeka koposa.+

      Waponyera m’nyanja mahatchi ndi okwera pamahatchiwo.”+

  • Oweruza 5:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Inu Yehova, adani anu onse afafanizidwe chimodzimodzi,+

      Ndipo okukondani inu+ akhale amphamvu ngati mmene dzuwa limakhalira.”+

      Choncho, dzikolo linakhala pa mtendere zaka 40.+

  • Esitere 9:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Anawalamula kuti masiku amenewa akhale ochita phwando, kusangalala, kutumizirana chakudya+ ndi kupereka mphatso kwa anthu osauka.+ Anatero pakuti amenewa ndi masiku amene Ayuda anasiya kuvutitsidwa ndi adani awo,+ komanso mwezi umene chisoni chawo chinasintha kukhala chikondwerero ndiponso pamene tsiku lolira+ linasintha kukhala tsiku losangalala.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena