Esitere 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakati pa Ayuda panali chisangalalo, kukondwa+ ndi kunyadira ndipo anthu anali kuwapatsa ulemu. Miyambo 28:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Anthu olungama akamasangalala+ zimakhala bwino kwambiri, koma anthu oipa akamalamulira, munthu amadzisintha maonekedwe.+
12 Anthu olungama akamasangalala+ zimakhala bwino kwambiri, koma anthu oipa akamalamulira, munthu amadzisintha maonekedwe.+