Genesis 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zinatero pakuti Yehova anachititsa kuti akazi onse a m’nyumba ya Abimeleki asabereke, chifukwa cha Sara mkazi wa Abulahamu.+ Genesis 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Potsirizira pake, Mulungu anakumbukira Rakele ndipo anamumvera n’kumuyankha mwa kum’patsa mphamvu zobereka.+ 1 Samueli 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 koma Hana anangom’patsa gawo limodzi. Komabe, iye anali kukonda kwambiri Hana+ ngakhale kuti Yehova anali atatseka mimba yake.+
18 Zinatero pakuti Yehova anachititsa kuti akazi onse a m’nyumba ya Abimeleki asabereke, chifukwa cha Sara mkazi wa Abulahamu.+
22 Potsirizira pake, Mulungu anakumbukira Rakele ndipo anamumvera n’kumuyankha mwa kum’patsa mphamvu zobereka.+
5 koma Hana anangom’patsa gawo limodzi. Komabe, iye anali kukonda kwambiri Hana+ ngakhale kuti Yehova anali atatseka mimba yake.+