Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 15:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno Abisalomu anali kupitiriza kunena kuti: “Haa! Zikanakhalatu bwino ndikanaikidwa kukhala woweruza m’dziko lino+ kuti munthu aliyense wokhala ndi mlandu kapena wofuna chiweruzo azibwera kwa ine, ndipo ndikanamuchitira chilungamo.”+

  • Esitere 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ndiyeno Hamani anayamba kudzitamandira pamaso pawo chifukwa cha kuchuluka kwa chuma chake+ ndi kuchuluka kwa ana ake aamuna.+ Anadzitamandiranso chifukwa cha zonse zimene mfumu inamulemekeza nazo komanso chifukwa chakuti inamukweza kuposa akalonga ndi atumiki a mfumu.+

  • Miyambo 26:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Kodi waona munthu wodziona ngati wanzeru m’maso mwake?+ Munthu wopusa ali ndi chiyembekezo chachikulu+ kuposa iyeyo.

  • Aroma 12:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Muziona ena mmene inuyo mumadzionera.+ Musamaganize modzikweza,+ koma khalani ndi mtima wodzichepetsa.+ Musadziyese anzeru.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena