Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 39:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Anawombanso lamba wa pamimba+ ndi ulusi wopota wabwino kwambiri, ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wonyika mu utoto wofiirira ndi ulusi wofiira kwambiri, monga mmene Yehova analamulira Mose.

  • Esitere 8:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno Moredekai anachoka pamaso pa mfumu atavala chovala chachifumu+ cha buluu ndi nsalu yoyera. Analinso atavala chisoti chachikulu chachifumu chagolide, mkanjo wa nsalu yabwino kwambiri yaubweya wa nkhosa+ wonyika mu utoto wofiirira.+ Ndipo mumzinda wa Susani munamveka kufuula kwa chisangalalo ndi kukondwera.+

  • Machitidwe 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pamenepo panali mayi wina dzina lake Lidiya ndipo anali wolambira Mulungu. Iyeyu anali wochokera kumzinda wa Tiyatira+ ndipo anali wogulitsa nsalu ndi zovala zofiirira. Pamene anali kumvetsera, Yehova anatsegula kwambiri mtima wake+ kuti atchere khutu ku zimene Paulo anali kunena.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena