Deuteronomo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Mudziikire oweruza+ ndi atsogoleri+ m’mizinda yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, malinga ndi mafuko anu. Oweruza ndi atsogoleriwo aziweruza anthu ndi chiweruzo cholungama. Rute 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Zitatero, Boazi anapita kuchipata.+ Kumeneko iye anakhala pansi. Ali chikhalire choncho, anaona wowombola anam’tchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe Uje takhotera pano, khala pansi apa.” Motero anakhota n’kukhala pansi. Yobu 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndikapita kuchipata cha mzinda,+Ndinkakonzako malo anga okhala pabwalo la mzinda.+
18 “Mudziikire oweruza+ ndi atsogoleri+ m’mizinda yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, malinga ndi mafuko anu. Oweruza ndi atsogoleriwo aziweruza anthu ndi chiweruzo cholungama.
4 Zitatero, Boazi anapita kuchipata.+ Kumeneko iye anakhala pansi. Ali chikhalire choncho, anaona wowombola anam’tchula uja+ akudutsa. Ndiyeno Boazi anati: “Iwe Uje takhotera pano, khala pansi apa.” Motero anakhota n’kukhala pansi.