Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 31:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ana awo amene sadziwa chilamulo ichi azimvetsera,+ ndipo aphunzire kuopa Yehova Mulungu wanu masiku onse amene mudzakhala panthaka imene mukupita kukaitenga kukhala yanu,+ mutawoloka Yorodano.”

  • Deuteronomo 32:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Malangizo anga adzagwa ngati mvula,+

      Mawu anga adzatsika ngati mame,+

      Ngati mvula yowaza pa udzu,+

      Ngatinso mvula yamphamvu pazomera.+

  • 1 Timoteyo 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chifukwa chopereka malangizo awa kwa abale, udzakhala mtumiki wabwino wa Khristu Yesu. Ndipo udzakula bwino ndi mawu a chikhulupiriro ndiponso chiphunzitso chabwino+ chimene wachitsatira mosamala.+

  • Tito 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 wogwira mwamphamvu mawu okhulupirika pamene akuphunzitsa mwaluso,+ kuti athe kulimbikitsa anthu ndi chiphunzitso cholondola+ ndiponso kudzudzula+ otsutsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena