Ezekieli 18:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tayani zolakwa zanu zonse zimene munachita+ ndipo muyesetse kukhala ndi mtima watsopano+ ndiponso mzimu watsopano.+ Kodi muferenji+ inu a nyumba ya Isiraeli?’ Aefeso 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 kuti muvule umunthu wakale+ umene umagwirizana ndi khalidwe lanu lakale, umenenso ukuipitsidwa+ malinga ndi zilakolako zonyenga za umunthuwo.+ Yakobo 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho siyani khalidwe lililonse lonyansa ndiponso siyani khalidwe lochita zoipa, lomwe ndi losafunika,+ ndipo vomerezani mofatsa mawu okhoza kupulumutsa miyoyo yanu,+ kuti abzalidwe mwa inu.+
31 Tayani zolakwa zanu zonse zimene munachita+ ndipo muyesetse kukhala ndi mtima watsopano+ ndiponso mzimu watsopano.+ Kodi muferenji+ inu a nyumba ya Isiraeli?’
22 kuti muvule umunthu wakale+ umene umagwirizana ndi khalidwe lanu lakale, umenenso ukuipitsidwa+ malinga ndi zilakolako zonyenga za umunthuwo.+
21 Choncho siyani khalidwe lililonse lonyansa ndiponso siyani khalidwe lochita zoipa, lomwe ndi losafunika,+ ndipo vomerezani mofatsa mawu okhoza kupulumutsa miyoyo yanu,+ kuti abzalidwe mwa inu.+