Miyambo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kudzakupulumutsa kwa mkazi wachilendo, mkazi wochokera kwina+ wolankhula mwaukathyali,+ Miyambo 7:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mkaziyo wamusocheretsa mnyamatayo pochita zinthu zambiri zomukopa.+ Wamunyengerera ndi milomo yake yotulutsa mawu okopa.+
21 Mkaziyo wamusocheretsa mnyamatayo pochita zinthu zambiri zomukopa.+ Wamunyengerera ndi milomo yake yotulutsa mawu okopa.+