Miyambo 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kudzakupulumutsa kwa mkazi wachilendo, mkazi wochokera kwina+ wolankhula mwaukathyali,+ Miyambo 7:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mwadzidzidzi mnyamatayo wayamba kulondola mkaziyo+ ngati ng’ombe yamphongo yopita kokaphedwa, ndiponso ngati kuti wamangidwa m’matangadza kuti alandire chilango* cha munthu wopusa. Miyambo 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakamwa pa akazi achilendo pali ngati dzenje lakuya.+ Wotsutsidwa ndi Yehova adzagweramo.+ Miyambo 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti hule lili ngati dzenje lakuya,+ ndipo mkazi wachilendo ali ngati chitsime chopapatiza.
22 Mwadzidzidzi mnyamatayo wayamba kulondola mkaziyo+ ngati ng’ombe yamphongo yopita kokaphedwa, ndiponso ngati kuti wamangidwa m’matangadza kuti alandire chilango* cha munthu wopusa.