Numeri 16:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma ngati angafe ndi chinthu chachilendo chimene Yehova achite,+ kuti nthaka iyasame n’kuwameza iwo+ ndi zonse ali nazo, moti iwo n’kutsikira ku Manda*+ ali amoyo, pamenepo mudziwa ndithu kuti amunawa anyoza+ Yehova.” Numeri 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zitatero, nthaka inayasama n’kuwameza.+ Koma Kora anafa pamene moto unanyeketsa gulu la amuna 250.+ Choncho iwowa anakhala chitsanzo chopereka chenjezo.+
30 Koma ngati angafe ndi chinthu chachilendo chimene Yehova achite,+ kuti nthaka iyasame n’kuwameza iwo+ ndi zonse ali nazo, moti iwo n’kutsikira ku Manda*+ ali amoyo, pamenepo mudziwa ndithu kuti amunawa anyoza+ Yehova.”
10 Zitatero, nthaka inayasama n’kuwameza.+ Koma Kora anafa pamene moto unanyeketsa gulu la amuna 250.+ Choncho iwowa anakhala chitsanzo chopereka chenjezo.+