Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yohane 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Zinthu zonse zinakhalako kudzera mwa iye,+ ndipo palibe chinthu ngakhale chimodzi chimene chinakhalapo popanda iyeyo.

  • Yohane 8:58
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 58 Yesu anati: “Ndithudi ndikukuuzani, Abulahamu asanakhaleko, ine n’kuti ndilipo kale.”+

  • Yohane 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndipo tsopano Atate, ndiloleni kuti ndikhale pambali panu, ndipo mundipatse ulemerero umene ndinali nawo pambali panu dziko lisanakhalepo.+

  • Akolose 1:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 chifukwa kudzera mwa iye+ zinthu zina zonse zinalengedwa, zakumwamba ndi zapadziko lapansi. Inde, zinthu zooneka ndi zinthu zosaoneka, kaya ndi mipando yachifumu, kapena ambuye, kapena maboma, kapena maulamuliro.+ Zinthu zina zonse zinalengedwa kudzera mwa iye,+ ndiponso chifukwa cha iye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena