Salimo 37:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pakamwa pa munthu wolungama pamalankhula zinthu zanzeru,+Ndipo lilime lake limalankhula zinthu zachilungamo.+ Miyambo 11:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zipatso za munthu wolungama ndizo mtengo wa moyo,+ ndipo munthu wopulumutsa miyoyo ndi wanzeru.+ Mateyu 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chake chabwino,+ koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa.+ Yakobo 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 dziwani kuti amene wabweza wochimwa panjira yake yoipa,+ adzapulumutsa moyo wa wochimwayo ku imfa+ ndipo adzakwirira machimo ambiri.+
30 Pakamwa pa munthu wolungama pamalankhula zinthu zanzeru,+Ndipo lilime lake limalankhula zinthu zachilungamo.+
35 Munthu wabwino amatulutsa zabwino m’chuma chake chabwino,+ koma munthu woipa amatulutsa zoipa m’chuma chake choipa.+
20 dziwani kuti amene wabweza wochimwa panjira yake yoipa,+ adzapulumutsa moyo wa wochimwayo ku imfa+ ndipo adzakwirira machimo ambiri.+