2 Mbiri 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yehova anapitiriza kutumiza aneneri+ pakati pawo kuti awabwezere kwa iye. Aneneriwo anapitiriza kupereka umboni wowatsutsa, koma sanamvere.+ Miyambo 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawiyo udzanena kuti: “Ndinkadana ndi malangizo* ine,+ ndipo mtima wanga sunkavomereza kudzudzula.+ Yohane 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Amene amachita zinthu zoipa+ amadana ndi kuwala ndipo safika pamene pali kuwala, kuti ntchito zake zisadzudzulidwe.+
19 Yehova anapitiriza kutumiza aneneri+ pakati pawo kuti awabwezere kwa iye. Aneneriwo anapitiriza kupereka umboni wowatsutsa, koma sanamvere.+
12 Pa nthawiyo udzanena kuti: “Ndinkadana ndi malangizo* ine,+ ndipo mtima wanga sunkavomereza kudzudzula.+
20 Amene amachita zinthu zoipa+ amadana ndi kuwala ndipo safika pamene pali kuwala, kuti ntchito zake zisadzudzulidwe.+