Mlaliki 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+ Ezekieli 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga.+ Moyo+ wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga.+ Moyo umene ukuchimwawo+ ndi umene udzafe.+
13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+
4 Tamverani! Miyoyo yonse ndi yanga.+ Moyo+ wa bambo komanso moyo wa mwana, yonse ndi yanga.+ Moyo umene ukuchimwawo+ ndi umene udzafe.+