Genesis 22:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno mngeloyo anapitiriza kulankhula kuti: “Usatambasulire dzanja lako mwanayo ndipo usam’chite kanthu kena kalikonse.+ Tsopano ndadziwa kuti ndiwe woopa Mulungu, pakuti sunakane kupereka kwa ine mwana wako mmodzi yekhayo.”+ 1 Samueli 30:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Palibe chinthu chawo chilichonse chimene chinasowa, ana aamuna kapena ana aakazi, ngakhalenso zinthu zimene anafunkha kwa iwo komanso chilichonse chimene anawatengera.+ Davide analanditsa zonsezo.
12 Ndiyeno mngeloyo anapitiriza kulankhula kuti: “Usatambasulire dzanja lako mwanayo ndipo usam’chite kanthu kena kalikonse.+ Tsopano ndadziwa kuti ndiwe woopa Mulungu, pakuti sunakane kupereka kwa ine mwana wako mmodzi yekhayo.”+
19 Palibe chinthu chawo chilichonse chimene chinasowa, ana aamuna kapena ana aakazi, ngakhalenso zinthu zimene anafunkha kwa iwo komanso chilichonse chimene anawatengera.+ Davide analanditsa zonsezo.