Yobu 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu amene watsala pangʼono kufa ankandidalitsa,+Ndipo ndinkasangalatsa mtima wa mkazi wamasiye.+
13 Munthu amene watsala pangʼono kufa ankandidalitsa,+Ndipo ndinkasangalatsa mtima wa mkazi wamasiye.+