Salimo 119:163 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 163 Ndimadana ndi chinyengo+ ndipo chimandinyansa,+Koma ndimakonda chilamulo chanu.+ Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+ Miyambo 30:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zachinyengo ndi mawu onama muwaike kutali ndi ine.+ Musandipatse umphawi kapena chuma.+ Ndidye chakudya chimene ndikufunika kudya,+ Aefeso 4:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+
8 Zachinyengo ndi mawu onama muwaike kutali ndi ine.+ Musandipatse umphawi kapena chuma.+ Ndidye chakudya chimene ndikufunika kudya,+
25 Chotero, popeza tsopano mwataya chinyengo,+ aliyense wa inu alankhule zoona kwa mnzake,+ chifukwa ndife ziwalo za thupi limodzi.+