Yobu 28:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mwala wamtengo wapatali wa korali+ ndi wa kulusitalo sizingayerekezedwe n’komwe ndi nzeruzo.Ndipo thumba lodzaza ndi nzeru ndi lamtengo wapatali kuposa thumba lodzaza ndi ngale.+
18 Mwala wamtengo wapatali wa korali+ ndi wa kulusitalo sizingayerekezedwe n’komwe ndi nzeruzo.Ndipo thumba lodzaza ndi nzeru ndi lamtengo wapatali kuposa thumba lodzaza ndi ngale.+