1 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Munthu akakuchitirani choipa musamabwezere ndi choipa,+ akakuchitirani chipongwe musamabwezere ndi chipongwe.+ Mʼmalomwake muziwachitira zabwino*+ chifukwa Mulungu anakusankhani kuti muzidalitsa ena kuti nayenso adzakudalitseni. 1 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:9 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 195
9 Munthu akakuchitirani choipa musamabwezere ndi choipa,+ akakuchitirani chipongwe musamabwezere ndi chipongwe.+ Mʼmalomwake muziwachitira zabwino*+ chifukwa Mulungu anakusankhani kuti muzidalitsa ena kuti nayenso adzakudalitseni.