Deuteronomo 12:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Yehova Mulungu wako akadzafutukula malire a dziko lako+ monga mmene wakulonjezera,+ ndipo iwe n’kudzanena kuti, ‘Ndikufuna kudya nyama,’ chifukwa walakalaka kudya nyama, nthawi iliyonse imene mtima wako walakalaka kudya nyama uzidzadya.+ Salimo 78:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Chifukwa cha iwo anachotsa mitundu ina pang’onopang’ono m’dzikoli,+Ndipo anayesa dzikoli ndi kuligawa kwa iwo kukhala cholowa chawo,+Moti anachititsa mafuko a Isiraeli kukhala m’nyumba zawozawo.+
20 “Yehova Mulungu wako akadzafutukula malire a dziko lako+ monga mmene wakulonjezera,+ ndipo iwe n’kudzanena kuti, ‘Ndikufuna kudya nyama,’ chifukwa walakalaka kudya nyama, nthawi iliyonse imene mtima wako walakalaka kudya nyama uzidzadya.+
55 Chifukwa cha iwo anachotsa mitundu ina pang’onopang’ono m’dzikoli,+Ndipo anayesa dzikoli ndi kuligawa kwa iwo kukhala cholowa chawo,+Moti anachititsa mafuko a Isiraeli kukhala m’nyumba zawozawo.+