Miyambo 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 chifukwa kupeza nzeru monga phindu n’kwabwino kuposa kupeza siliva monga phindu, ndipo kukhala nazo monga zokolola n’kwabwino kuposa kukhala ndi golide.+ Miyambo 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nzeru ndiyo chinthu chofunika kwambiri.+ Peza nzeru, ndipo pa zinthu zonse zimene upeze, upezenso luso lomvetsa zinthu.+
14 chifukwa kupeza nzeru monga phindu n’kwabwino kuposa kupeza siliva monga phindu, ndipo kukhala nazo monga zokolola n’kwabwino kuposa kukhala ndi golide.+
7 Nzeru ndiyo chinthu chofunika kwambiri.+ Peza nzeru, ndipo pa zinthu zonse zimene upeze, upezenso luso lomvetsa zinthu.+