Yobu 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Golide woyenga bwino sangaperekedwe mosinthana nazo,+Ndipo sangayeze siliva monga mtengo wake. Miyambo 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+ Miyambo 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kupeza nzeru n’kwabwino kwambiri kuposa kupeza golide.+ Ndipo ndi bwino kusankha kumvetsa zinthu kuposa siliva.+
10 Landirani malangizo* anga osati siliva, ndiponso kudziwa zinthu m’malo mwa golide wabwino kwambiri.+
16 Kupeza nzeru n’kwabwino kwambiri kuposa kupeza golide.+ Ndipo ndi bwino kusankha kumvetsa zinthu kuposa siliva.+