Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mlaliki 12:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Wosonkhanitsayo anafufuza mawu okoma+ ndipo analemba mawu olondola a choonadi.+

  • Luka 4:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Pamenepo onse anayamba kumutamanda ndi kudabwa ndi mawu ogwira mtima+ otuluka pakamwa pake, mwakuti anali kunena kuti: “Kodi iyeyu si mwana wa Yosefe?”+

  • 2 Akorinto 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Choncho popeza timaopa+ Ambuye, tikupitiriza kukopa+ anthu. Mulungu akudziwa bwino zolinga zathu. Koma ndili ndi chikhulupiriro kuti inunso, mwachikumbumtima chanu, mukudziwa bwino zolinga zathu.+

  • Akolose 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Nthawi zonse mawu anu azikhala achisomo,+ okoma ngati kuti mwawathira mchere,+ kuti mudziwe mmene mungayankhire+ wina aliyense.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena