Miyambo 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mimba ya munthu imakhuta zipatso za pakamwa pake.+ Iye amakhuta ngakhale zokolola za milomo yake.+ Mlaliki 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ntchito yonse imene anthu amaigwira mwakhama amagwirira pakamwa pawo,+ koma moyo wawo sukhuta.
20 Mimba ya munthu imakhuta zipatso za pakamwa pake.+ Iye amakhuta ngakhale zokolola za milomo yake.+