Genesis 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+ Miyambo 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Munthu wakhama amadzigwirira yekha ntchito+ chifukwa chakuti pakamwa pake pamamukakamiza kwambiri.+
19 Udzadya chakudya kuchokera m’thukuta la nkhope yako mpaka utabwerera kunthaka, pakuti n’kumene unatengedwa.+ Popeza ndiwe fumbi, kufumbiko udzabwerera.”+
26 Munthu wakhama amadzigwirira yekha ntchito+ chifukwa chakuti pakamwa pake pamamukakamiza kwambiri.+