Salimo 37:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zinthu zochepa za munthu wolungama ndi zabwino+Kusiyana ndi zinthu zochuluka za anthu ambiri oipa.+ Miyambo 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa ukuopa Yehova,+ kusiyana ndi kukhala ndi zinthu zambiri koma uli ndi nkhawa.+ Miyambo 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndi bwino kudya zamasamba koma pali chikondi,+ kusiyana ndi kudya nyama ya ng’ombe yamphongo yodyetsedwa bwino pali chidani.+
16 Zinthu zochepa za munthu wolungama ndi zabwino+Kusiyana ndi zinthu zochuluka za anthu ambiri oipa.+
16 Ndi bwino kukhala ndi zinthu zochepa ukuopa Yehova,+ kusiyana ndi kukhala ndi zinthu zambiri koma uli ndi nkhawa.+
17 Ndi bwino kudya zamasamba koma pali chikondi,+ kusiyana ndi kudya nyama ya ng’ombe yamphongo yodyetsedwa bwino pali chidani.+