Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Chivumbulutso 11:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Koma mitundu ya anthu inakwiya, ndipo mkwiyo wanu unafika. Inafikanso nthawi yoikidwiratu yakuti akufa aweruzidwe, nthawi yopereka mphoto+ kwa akapolo anu aneneri,+ ndiponso kwa oyerawo, ndi oopa dzina lanu, olemekezeka ndi onyozeka omwe.+ Komanso, nthawi yowononga+ amene akuwononga dziko lapansi.”+

  • Chivumbulutso 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndipo anamuponyera m’phompho+ ndi kutseka pakhomo pa phompholo n’kuikapo chidindo kuti asasocheretsenso mitundu ya anthu kufikira zitatha zaka 1,000. Pambuyo pake, adzamasulidwa kanthawi kochepa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena