Yobu 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kumandako oipa asiya kusautsika,+Ndipo kumeneko anthu omwe mphamvu zawo zatha, akupuma.+ Mlaliki 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndinadana ndi moyo+ chifukwa ndinaona kuti ntchito imene yachitidwa padziko lapansi pano ndi yosautsa mtima.+ Pakuti zonse zinali zachabechabe ndipo kuchita zimenezi kunali ngati kuthamangitsa mphepo.+
17 Ine ndinadana ndi moyo+ chifukwa ndinaona kuti ntchito imene yachitidwa padziko lapansi pano ndi yosautsa mtima.+ Pakuti zonse zinali zachabechabe ndipo kuchita zimenezi kunali ngati kuthamangitsa mphepo.+