1 Mafumu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho atumiki ake anamuuza kuti: “Mbuyanga mfumu, anthu akufunireni namwali wamng’ono+ woti azisamalira+ inu mfumu. Akhale mlezi+ wanu woti azigona pafupi nanu+ ndipo mbuyanga mfumu muzitenthedwa.”+
2 Choncho atumiki ake anamuuza kuti: “Mbuyanga mfumu, anthu akufunireni namwali wamng’ono+ woti azisamalira+ inu mfumu. Akhale mlezi+ wanu woti azigona pafupi nanu+ ndipo mbuyanga mfumu muzitenthedwa.”+