Yobu 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kapena ngati pakati pomwe papita pachabe mosadziwa,+ bwenzi ine kulibe,Mofanana ndi ana amene sanaone kuwala.+ Mlaliki 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma amene ali bwino kuposa onsewa ndi amene sanabadwe,+ amene sanaone ntchito yosautsa mtima imene ikuchitika padziko lapansi pano.+
16 Kapena ngati pakati pomwe papita pachabe mosadziwa,+ bwenzi ine kulibe,Mofanana ndi ana amene sanaone kuwala.+
3 Koma amene ali bwino kuposa onsewa ndi amene sanabadwe,+ amene sanaone ntchito yosautsa mtima imene ikuchitika padziko lapansi pano.+