Salimo 58:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Woipayo amayenda ngati nkhono imene ikusungunuka.Iwo sadzaona dzuwa ngati mwana wa mayi amene wapita padera.+ Mlaliki 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngati munthu atabereka ana 100+ n’kukhala ndi moyo zaka zambirimbiri, masiku a moyo wake n’kukhala ochuluka,+ koma moyo wake osakhutira ndi zinthu zabwino,+ komanso osalowa m’manda,+ ndithu mwana amene anabadwa wakufa ali bwino kuposa iyeyu.+ Hoseya 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu Yehova, apatseni zimene mukuyenera kuwapatsa.+ Chititsani kuti mimba zawo zizipita padera+ ndiponso mabere awo afote.
8 Woipayo amayenda ngati nkhono imene ikusungunuka.Iwo sadzaona dzuwa ngati mwana wa mayi amene wapita padera.+
3 Ngati munthu atabereka ana 100+ n’kukhala ndi moyo zaka zambirimbiri, masiku a moyo wake n’kukhala ochuluka,+ koma moyo wake osakhutira ndi zinthu zabwino,+ komanso osalowa m’manda,+ ndithu mwana amene anabadwa wakufa ali bwino kuposa iyeyu.+
14 Inu Yehova, apatseni zimene mukuyenera kuwapatsa.+ Chititsani kuti mimba zawo zizipita padera+ ndiponso mabere awo afote.